1 Samueli 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho wansembeyo anamupatsa mkate wopatulika,+ chifukwa panalibe mkate wina koma mkate wachionetsero umene anauchotsa pamaso pa Yehova tsiku limenelo kuti aikepo watsopano. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:6 Yesu—Ndi Njira, tsa. 76 Nsanja ya Olonda,3/15/2005, tsa. 309/1/2002, tsa. 181/15/1987, ptsa. 22-23
6 Choncho wansembeyo anamupatsa mkate wopatulika,+ chifukwa panalibe mkate wina koma mkate wachionetsero umene anauchotsa pamaso pa Yehova tsiku limenelo kuti aikepo watsopano.
21:6 Yesu—Ndi Njira, tsa. 76 Nsanja ya Olonda,3/15/2005, tsa. 309/1/2002, tsa. 181/15/1987, ptsa. 22-23