1 Samueli 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa tsikuli, mmodzi wa atumiki a Sauli anali kumeneko chifukwa anali atamusunga pamaso pa Yehova. Dzina lake anali Doegi+ ndipo anali wa ku Edomu.+ Iye anali mkulu wa abusa a Sauli.
7 Pa tsikuli, mmodzi wa atumiki a Sauli anali kumeneko chifukwa anali atamusunga pamaso pa Yehova. Dzina lake anali Doegi+ ndipo anali wa ku Edomu.+ Iye anali mkulu wa abusa a Sauli.