1 Samueli 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Davide ananyamuka tsiku lomwelo ndipo anapitiriza kuthawa+ Sauli. Patapita nthawi anafika kwa Mfumu Akisi ya ku Gati.+
10 Davide ananyamuka tsiku lomwelo ndipo anapitiriza kuthawa+ Sauli. Patapita nthawi anafika kwa Mfumu Akisi ya ku Gati.+