1 Samueli 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atafika kumeneko, atumiki a Akisi ananena kuti: “Kodi ameneyu si Davide mfumu ya dziko la Isiraeli? Suja ankamuimbira nyimbo uku akuvina nʼkumati,‘Sauli wapha adani ake masauzande,Ndipo Davide wapha masauzande ambirimbiri.’”+
11 Atafika kumeneko, atumiki a Akisi ananena kuti: “Kodi ameneyu si Davide mfumu ya dziko la Isiraeli? Suja ankamuimbira nyimbo uku akuvina nʼkumati,‘Sauli wapha adani ake masauzande,Ndipo Davide wapha masauzande ambirimbiri.’”+