1 Samueli 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho anawasiya kuti azikhala ndi mfumu ya Mowabu, moti iwo anakhala kumeneko nthawi yonse imene Davide ankabisala kumalo ovuta kufikako.+
4 Choncho anawasiya kuti azikhala ndi mfumu ya Mowabu, moti iwo anakhala kumeneko nthawi yonse imene Davide ankabisala kumalo ovuta kufikako.+