1 Samueli 22:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Patapita nthawi, Gadi,+ yemwe anali mneneri, anauza Davide kuti: “Usakhalenso kumalo ovuta kufikako. Chokako kumeneko ndipo upite mʼdziko la Yuda.”+ Choncho Davide anachoka nʼkupita kunkhalango ya Hereti.
5 Patapita nthawi, Gadi,+ yemwe anali mneneri, anauza Davide kuti: “Usakhalenso kumalo ovuta kufikako. Chokako kumeneko ndipo upite mʼdziko la Yuda.”+ Choncho Davide anachoka nʼkupita kunkhalango ya Hereti.