1 Samueli 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sauli anamva kuti Davide ndi anthu amene anali naye apezeka. Pa nthawiyi Sauli anali ku Gibeya+ atakhala pansi pa mtengo wa bwemba, pamalo okwezeka. Iye anali ndi mkondo mʼmanja ndipo atumiki ake onse anali atamuzungulira.
6 Sauli anamva kuti Davide ndi anthu amene anali naye apezeka. Pa nthawiyi Sauli anali ku Gibeya+ atakhala pansi pa mtengo wa bwemba, pamalo okwezeka. Iye anali ndi mkondo mʼmanja ndipo atumiki ake onse anali atamuzungulira.