7 Kenako Sauli anauza atumiki akewo kuti: “Tamverani inu a fuko la Benjamini. Kodi mwana wa Jese+ nayenso adzakupatsani nonsenu minda ya mpesa ndi minda ya mbewu zina? Kodi nonsenu adzakuikani kukhala atsogoleri a magulu a anthu 1,000 ndi atsogoleri a magulu a anthu 100?+