8 Nonsenu mwandikonzera chiwembu. Pamene mwana wanga anachita pangano ndi mwana wa Jese,+ palibe amene anandiuza. Palibenso amene wandichitira chifundo nʼkundiuza kuti mwana wanga weniweni wachititsa mtumiki wanga kundibisalira ngati mmene zililimu.”