1 Samueli 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iye anaphanso anthu amumzinda wa Nobu+ womwe unali mzinda wa ansembe. Anapha amuna ndi akazi, ana ndi ana oyamwa omwe, ngʼombe ndi abulu komanso nkhosa.
19 Iye anaphanso anthu amumzinda wa Nobu+ womwe unali mzinda wa ansembe. Anapha amuna ndi akazi, ana ndi ana oyamwa omwe, ngʼombe ndi abulu komanso nkhosa.