1 Samueli 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma iwe khala ndi ine ndipo usachite mantha. Chifukwa aliyense amene akufunafuna moyo wako akufunafunanso moyo wanga, ndipo ndikuteteza.”+
23 Koma iwe khala ndi ine ndipo usachite mantha. Chifukwa aliyense amene akufunafuna moyo wako akufunafunanso moyo wanga, ndipo ndikuteteza.”+