1 Samueli 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Davide anafunsira kwa Yehova+ kuti: “Kodi ndipite kukapha Afilisiti?” Yehova anayankha Davide kuti: “Pita, ukaphe Afilisitiwo ndipo ukapulumutse Keila.”
2 Ndiyeno Davide anafunsira kwa Yehova+ kuti: “Kodi ndipite kukapha Afilisiti?” Yehova anayankha Davide kuti: “Pita, ukaphe Afilisitiwo ndipo ukapulumutse Keila.”