1 Samueli 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamene Abiyatara+ mwana wamwamuna wa Ahimeleki ankathawira kwa Davide ku Keila, anatenga efodi.