1 Samueli 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Davide anati: “Yehova Mulungu wa Isiraeli, ine mtumiki wanu ndamva kuti Sauli akufuna kubwera kuno ku Keila kudzawononga mzindawu chifukwa cha ine.+
10 Kenako Davide anati: “Yehova Mulungu wa Isiraeli, ine mtumiki wanu ndamva kuti Sauli akufuna kubwera kuno ku Keila kudzawononga mzindawu chifukwa cha ine.+