1 Samueli 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide ankakhala mʼmalo ovuta kufikako kumapiri mʼchipululu cha Zifi.+ Sauli ankafunafuna Davide nthawi zonse,+ koma Yehova sanamʼpereke mʼmanja mwake. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:14 Nsanja ya Olonda,12/15/2015, tsa. 10
14 Davide ankakhala mʼmalo ovuta kufikako kumapiri mʼchipululu cha Zifi.+ Sauli ankafunafuna Davide nthawi zonse,+ koma Yehova sanamʼpereke mʼmanja mwake.