1 Samueli 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamene Davide anali mʼchipululu cha Zifi ku Horesi, anadziwa kuti* Sauli ali mʼderalo ndipo akufunafuna moyo wake.
15 Pamene Davide anali mʼchipululu cha Zifi ku Horesi, anadziwa kuti* Sauli ali mʼderalo ndipo akufunafuna moyo wake.