1 Samueli 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako Yonatani mwana wa Sauli anapita kwa Davide ku Horesi ndipo anamuthandiza* kuti apeze mphamvu kuchokera kwa Yehova.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:16 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo, Nsanja ya Olonda,12/15/2015, tsa. 10
16 Kenako Yonatani mwana wa Sauli anapita kwa Davide ku Horesi ndipo anamuthandiza* kuti apeze mphamvu kuchokera kwa Yehova.+