1 Samueli 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako awiriwo anachita pangano+ pamaso pa Yehova ndipo Davide anakhalabe ku Horesi koma Yonatani anabwerera kwawo.
18 Kenako awiriwo anachita pangano+ pamaso pa Yehova ndipo Davide anakhalabe ku Horesi koma Yonatani anabwerera kwawo.