1 Samueli 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako amuna a ku Zifi anapita kwa Sauli ku Gibeya+ nʼkumuuza kuti: “Davide akubisalatu pafupi ndi ife+ kumalo ovuta kufikako ku Horesi,+ paphiri la Hakila+ lomwe lili kumʼmwera* kwa Yesimoni.*+
19 Kenako amuna a ku Zifi anapita kwa Sauli ku Gibeya+ nʼkumuuza kuti: “Davide akubisalatu pafupi ndi ife+ kumalo ovuta kufikako ku Horesi,+ paphiri la Hakila+ lomwe lili kumʼmwera* kwa Yesimoni.*+