1 Samueli 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mukafufuze nʼkudziwa malo onse obisika kumene iye akubisala, ndipo mukabwere ndi umboni. Kenako ndidzapita nanu ndipo ngati alidi kumeneko, ndidzamʼfufuza pakati pa anthu masauzande* a ku Yuda.”
23 Mukafufuze nʼkudziwa malo onse obisika kumene iye akubisala, ndipo mukabwere ndi umboni. Kenako ndidzapita nanu ndipo ngati alidi kumeneko, ndidzamʼfufuza pakati pa anthu masauzande* a ku Yuda.”