1 Samueli 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Zitatero Sauli anasiya kusakasaka Davide+ ndipo anabwerera kukamenyana ndi Afilisiti. Nʼchifukwa chake malowo anawapatsa dzina lakuti Thanthwe Logawanitsa.
28 Zitatero Sauli anasiya kusakasaka Davide+ ndipo anabwerera kukamenyana ndi Afilisiti. Nʼchifukwa chake malowo anawapatsa dzina lakuti Thanthwe Logawanitsa.