1 Samueli 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako, Sauli anafika kumakola a nkhosa amiyala mʼmbali mwa msewu, kumene kunali phanga. Iye analowa mʼphangamo kukadzithandiza. Pa nthawiyi nʼkuti Davide ndi amuna amene ankayenda naye atakhala pansi kumbuyo kwa phangalo pamalo osaonekera.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:3 Nsanja ya Olonda,11/1/1989, tsa. 16
3 Kenako, Sauli anafika kumakola a nkhosa amiyala mʼmbali mwa msewu, kumene kunali phanga. Iye analowa mʼphangamo kukadzithandiza. Pa nthawiyi nʼkuti Davide ndi amuna amene ankayenda naye atakhala pansi kumbuyo kwa phangalo pamalo osaonekera.+