1 Samueli 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma kenako Davide anayamba kuvutika mumtima*+ chifukwa anadula kansalu kamʼmunsi mwa mkanjo wodula manja wa Sauli. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:5 Mulungu Azikukondani, tsa. 18 Nsanja ya Olonda,10/15/2007, tsa. 22
5 Koma kenako Davide anayamba kuvutika mumtima*+ chifukwa anadula kansalu kamʼmunsi mwa mkanjo wodula manja wa Sauli.