1 Samueli 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anauza anthu amene anali naye kuti: “Ndikaiona nkhaniyi mmene Yehova akuionera, ndikuona kuti sindingayerekeze kuchitira zimenezo mbuye wanga, wodzozedwa wa Yehova. Sindingamuchitire zoipa chifukwa iye ndi wodzozedwa wa Yehova.”+
6 Iye anauza anthu amene anali naye kuti: “Ndikaiona nkhaniyi mmene Yehova akuionera, ndikuona kuti sindingayerekeze kuchitira zimenezo mbuye wanga, wodzozedwa wa Yehova. Sindingamuchitire zoipa chifukwa iye ndi wodzozedwa wa Yehova.”+