1 Samueli 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nayenso Davide anatuluka mʼphangamo ndipo anaitana Sauli kuti: “Mbuyanga mfumu!”+ Sauli atatembenuka, Davide anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake kufika pansi.
8 Nayenso Davide anatuluka mʼphangamo ndipo anaitana Sauli kuti: “Mbuyanga mfumu!”+ Sauli atatembenuka, Davide anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake kufika pansi.