1 Samueli 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno Davide anauza Sauli kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukumvera zimene anthu akunena zakuti, ‘Davide akufuna kukuchitirani zoipa?’+
9 Ndiyeno Davide anauza Sauli kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukumvera zimene anthu akunena zakuti, ‘Davide akufuna kukuchitirani zoipa?’+