1 Samueli 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Lero mwaona nokha kuti Yehova anakuperekani mʼmanja mwanga mʼphangamu. Winawake anandiuza kuti ndikupheni,+ koma ndinakumverani chisoni nʼkunena kuti, ‘Sindingachitire zoipa mbuyanga, chifukwa ndi wodzozedwa wa Yehova.’+
10 Lero mwaona nokha kuti Yehova anakuperekani mʼmanja mwanga mʼphangamu. Winawake anandiuza kuti ndikupheni,+ koma ndinakumverani chisoni nʼkunena kuti, ‘Sindingachitire zoipa mbuyanga, chifukwa ndi wodzozedwa wa Yehova.’+