1 Samueli 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova akhale woweruza, ndipo aweruze pakati pa ine ndi inu. Iye adzaona nkhaniyi nʼkundiweruza kuti ndine wosalakwa+ ndipo adzandipulumutsa mʼmanja mwanu.”
15 Yehova akhale woweruza, ndipo aweruze pakati pa ine ndi inu. Iye adzaona nkhaniyi nʼkundiweruza kuti ndine wosalakwa+ ndipo adzandipulumutsa mʼmanja mwanu.”