1 Samueli 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Davide atangomaliza kulankhula mawu amenewa, Sauli anati: “Kodi ndi mawu ako, mwana wanga Davide?”+ Kenako Sauli anayamba kulira mokweza.
16 Davide atangomaliza kulankhula mawu amenewa, Sauli anati: “Kodi ndi mawu ako, mwana wanga Davide?”+ Kenako Sauli anayamba kulira mokweza.