1 Samueli 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anauza Davide kuti: “Ndiwe wolungama kwambiri kuposa ine, chifukwa wandichitira zabwino, koma ine ndakubwezera zoipa.+
17 Iye anauza Davide kuti: “Ndiwe wolungama kwambiri kuposa ine, chifukwa wandichitira zabwino, koma ine ndakubwezera zoipa.+