1 Samueli 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndi ndani amene angapeze mdani wake nʼkumusiya kuti apite mwamtendere? Yehova adzakupatsa zinthu zabwino+ chifukwa cha zimene wandichitira lero.
19 Ndi ndani amene angapeze mdani wake nʼkumusiya kuti apite mwamtendere? Yehova adzakupatsa zinthu zabwino+ chifukwa cha zimene wandichitira lero.