1 Samueli 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ine ndikudziwa kuti iweyo udzakhala mfumu,+ ndipo ufumu wa Isiraeli udzakhalabe mʼmanja mwako.