1 Samueli 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Patapita nthawi, Samueli+ anamwalira. Aisiraeli onse anasonkhana kuti alire maliro ake ndipo anamuika mʼmanda kunyumba kwake ku Rama.+ Kenako Davide ananyamuka nʼkupita kuchipululu cha Parana.
25 Patapita nthawi, Samueli+ anamwalira. Aisiraeli onse anasonkhana kuti alire maliro ake ndipo anamuika mʼmanda kunyumba kwake ku Rama.+ Kenako Davide ananyamuka nʼkupita kuchipululu cha Parana.