1 Samueli 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Panali munthu wina amene ankakhala ku Maoni,+ koma ntchito yake ankagwirira ku Karimeli.*+ Munthu ameneyu anali wolemera kwambiri ndipo anali ndi nkhosa 3,000 komanso mbuzi 1,000. Pa nthawiyi, iye ankameta ubweya wa nkhosa zake ku Karimeli. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:2 Tsanzirani, ptsa. 77-78 Nsanja ya Olonda,7/1/2009, tsa. 19
2 Panali munthu wina amene ankakhala ku Maoni,+ koma ntchito yake ankagwirira ku Karimeli.*+ Munthu ameneyu anali wolemera kwambiri ndipo anali ndi nkhosa 3,000 komanso mbuzi 1,000. Pa nthawiyi, iye ankameta ubweya wa nkhosa zake ku Karimeli.