1 Samueli 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Munthuyu dzina lake linali Nabala+ ndipo mkazi wake anali Abigayeli.+ Mkazi wakeyu anali wanzeru ndiponso wokongola, koma mwamunayu anali wouma mtima komanso wopanda khalidwe.+ Iye anali wakubanja la Kalebe.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:3 Tsanzirani, ptsa. 76-77 Nsanja ya Olonda,7/1/2009, ptsa. 18-19
3 Munthuyu dzina lake linali Nabala+ ndipo mkazi wake anali Abigayeli.+ Mkazi wakeyu anali wanzeru ndiponso wokongola, koma mwamunayu anali wouma mtima komanso wopanda khalidwe.+ Iye anali wakubanja la Kalebe.+