1 Samueli 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako mukamuuze kuti, ‘Mukhale ndi moyo wautali komanso wabwino.* Anthu onse amʼnyumba yanu akhale ndi moyo wabwino limodzi ndi zonse zimene muli nazo.
6 Kenako mukamuuze kuti, ‘Mukhale ndi moyo wautali komanso wabwino.* Anthu onse amʼnyumba yanu akhale ndi moyo wabwino limodzi ndi zonse zimene muli nazo.