1 Samueli 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndamva kuti mukumeta ubweya wa nkhosa zanu. Pamene abusa anu anali ndi ife, sitinawachitire choipa chilichonse,+ ndipo pa nthawi yonse imene anali ku Karimeli, palibe chinthu chawo chimene chinasowa. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:7 Tsanzirani, tsa. 78 Nsanja ya Olonda,7/1/2009, tsa. 19
7 Ndamva kuti mukumeta ubweya wa nkhosa zanu. Pamene abusa anu anali ndi ife, sitinawachitire choipa chilichonse,+ ndipo pa nthawi yonse imene anali ku Karimeli, palibe chinthu chawo chimene chinasowa.