1 Samueli 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Funsani anyamata anu zimenezi ndipo akuuzani. Ndikupempha kuti muwakomere mtima anyamata anga chifukwa tabwera pa nthawi yachisangalalo.* Chonde mugawire atumiki anu ndi ine mwana wanu Davide chilichonse chimene mungakonde kutipatsa.’”+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:8 Tsanzirani, tsa. 78 Nsanja ya Olonda,7/1/2009, tsa. 19
8 Funsani anyamata anu zimenezi ndipo akuuzani. Ndikupempha kuti muwakomere mtima anyamata anga chifukwa tabwera pa nthawi yachisangalalo.* Chonde mugawire atumiki anu ndi ine mwana wanu Davide chilichonse chimene mungakonde kutipatsa.’”+