1 Samueli 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nabala anawayankha kuti: “Kodi Davide ndi ndani, ndipo mwana wa Jese ndi ndani? Masiku ano atumiki ambiri akukonda kuthawa ambuye awo.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:10 Tsanzirani, tsa. 78 Nsanja ya Olonda,7/1/2009, tsa. 19
10 Nabala anawayankha kuti: “Kodi Davide ndi ndani, ndipo mwana wa Jese ndi ndani? Masiku ano atumiki ambiri akukonda kuthawa ambuye awo.+