-
1 Samueli 25:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndiye zoona ine nditenge mkate wanga, madzi ndi nyama imene ndaphera antchito anga ometa ubweya wa nkhosa nʼkupereka kwa amuna amene sindikudziwa kumene achokera?”
-