1 Samueli 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Izi zili choncho, mmodzi wa antchito a Nabala anauza Abigayeli, mkazi wa Nabala kuti: “Davide anatuma anthu kuchokera kuchipululu kudzafunira zabwino abwana, koma abwanawo awalalatira.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:14 Tsanzirani, ptsa. 76-79 Nsanja ya Olonda,7/1/2009, ptsa. 18-20
14 Izi zili choncho, mmodzi wa antchito a Nabala anauza Abigayeli, mkazi wa Nabala kuti: “Davide anatuma anthu kuchokera kuchipululu kudzafunira zabwino abwana, koma abwanawo awalalatira.+