1 Samueli 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu amenewa anatichitira zabwino kwambiri ndipo sanatichitire choipa chilichonse. Pa nthawi yonse imene tinali nawo kutchire, palibe chinthu chathu chimene chinasowa.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:15 Tsanzirani, tsa. 78 Nsanja ya Olonda,7/1/2009, tsa. 19
15 Anthu amenewa anatichitira zabwino kwambiri ndipo sanatichitire choipa chilichonse. Pa nthawi yonse imene tinali nawo kutchire, palibe chinthu chathu chimene chinasowa.+