1 Samueli 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiye muona zimene mungachite, chifukwa zimenezi zibweretsa tsoka kwa abwana ndi anthu onse amʼnyumba yawo.+ Abwana athu ndi munthu wopanda pake+ ndipo palibe amene angalankhule nawo.” 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:17 Tsanzirani, tsa. 79 Nsanja ya Olonda,7/1/2009, tsa. 20
17 Ndiye muona zimene mungachite, chifukwa zimenezi zibweretsa tsoka kwa abwana ndi anthu onse amʼnyumba yawo.+ Abwana athu ndi munthu wopanda pake+ ndipo palibe amene angalankhule nawo.”