1 Samueli 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Davide anali atanena kuti: “Ndinagwira ntchito pachabe polondera zinthu za munthu ameneyu mʼchipululu ndipo palibe chinthu chake ngakhale chimodzi chimene chinasowa.+ Koma akundibwezera zoipa pa zabwino zimene ndinamʼchitira.+
21 Davide anali atanena kuti: “Ndinagwira ntchito pachabe polondera zinthu za munthu ameneyu mʼchipululu ndipo palibe chinthu chake ngakhale chimodzi chimene chinasowa.+ Koma akundibwezera zoipa pa zabwino zimene ndinamʼchitira.+