1 Samueli 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho Mulungu alange mowirikiza adani a Davide,* ngati ine ndidzasiya mwamuna* aliyense wa mʼnyumba ya Nabala ali ndi moyo mpaka mʼmawa.”
22 Choncho Mulungu alange mowirikiza adani a Davide,* ngati ine ndidzasiya mwamuna* aliyense wa mʼnyumba ya Nabala ali ndi moyo mpaka mʼmawa.”