-
1 Samueli 25:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Kenako anawerama pamapazi a Davide nʼkunena kuti: “Mbuyanga, zolakwa zonse zikhale pa ine. Lolani kuti ine kapolo wanu wamkazi ndilankhule nanu ndipo mvetserani zimene kapolo wanu akufuna kunena.
-