1 Samueli 25:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chonde mbuyanga, musaganizire za Nabala, munthu wopanda pake,+ chifukwa zochita zake nʼzogwirizana ndi dzina lake. Dzina lake ndi Nabala* ndipo ndi wopandadi nzeru. Koma ine kapolo wanu sindinawaone anyamata amene inu mbuyanga munawatuma. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:25 Tsanzirani, tsa. 80 Nsanja ya Olonda,7/1/2009, ptsa. 20-21
25 Chonde mbuyanga, musaganizire za Nabala, munthu wopanda pake,+ chifukwa zochita zake nʼzogwirizana ndi dzina lake. Dzina lake ndi Nabala* ndipo ndi wopandadi nzeru. Koma ine kapolo wanu sindinawaone anyamata amene inu mbuyanga munawatuma.