1 Samueli 25:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chonde, khululukani machimo a ine kapolo wanu wamkazi, chifukwa mosakayikira Yehova adzachititsa kuti nyumba ya mbuyanga ikhazikike,+ chifukwa inu mbuyanga mukumenya nkhondo za Yehova.+ Ndipo pa moyo wanu simunapezekepo ndi choipa chilichonse.+
28 Chonde, khululukani machimo a ine kapolo wanu wamkazi, chifukwa mosakayikira Yehova adzachititsa kuti nyumba ya mbuyanga ikhazikike,+ chifukwa inu mbuyanga mukumenya nkhondo za Yehova.+ Ndipo pa moyo wanu simunapezekepo ndi choipa chilichonse.+