1 Samueli 25:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu akakuukirani ndi kufunafuna moyo wanu, Yehova Mulungu wanu adzakulunga moyo wanu mʼphukusi la moyo kuti utetezeke. Koma moyo wa adani anu adzauponya kutali ngati mmene munthu amaponyera mwala ndi gulaye.* 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:29 Nsanja ya Olonda,6/15/1991, tsa. 14
29 Munthu akakuukirani ndi kufunafuna moyo wanu, Yehova Mulungu wanu adzakulunga moyo wanu mʼphukusi la moyo kuti utetezeke. Koma moyo wa adani anu adzauponya kutali ngati mmene munthu amaponyera mwala ndi gulaye.*