1 Samueli 25:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 simudzadandaula kapena kuvutika mumtima kuti munakhetsa magazi popanda chifukwa, kapena chifukwa choti munabwezera* nokha ndi dzanja lanu.+ Yehova akadzakuchitirani zabwino mbuyanga, mudzandikumbukire ine kapolo wanu wamkazi.” 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:31 Tsanzirani, tsa. 80 Nsanja ya Olonda,7/1/2009, ptsa. 20-21
31 simudzadandaula kapena kuvutika mumtima kuti munakhetsa magazi popanda chifukwa, kapena chifukwa choti munabwezera* nokha ndi dzanja lanu.+ Yehova akadzakuchitirani zabwino mbuyanga, mudzandikumbukire ine kapolo wanu wamkazi.”